Ekisodo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno udzatenge mafuta odzozera+ ndi kudzoza chihema chopatulika ndi zonse zimene zili mkati mwake.+ Motero udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika. Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+
9 Ndiyeno udzatenge mafuta odzozera+ ndi kudzoza chihema chopatulika ndi zonse zimene zili mkati mwake.+ Motero udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+