Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+

  • 2 Mafumu 10:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kungoti iye sanasiye kutsatira machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ Machimo ake anali kulambira ana a ng’ombe agolide.+ Mmodzi wa ana a ng’ombe agolidewo anali ku Beteli, ndipo wina ku Dani.+

  • Salimo 106:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iwo anapanganso mwana wa ng’ombe ku Horebe,+

      Ndipo anaweramira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+

  • Hoseya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano anthu ake akuchita machimo ena ndipo akugwiritsa ntchito siliva wawo popanga zifanizo zachitsulo chosungunula.+ Zifanizo zimenezo ndi mafano opangidwa mogwirizana ndi maganizo awo,+ koma zonsezi ndi ntchito za amisiri.+ Iwo amauza mafanowo kuti, ‘Amuna opereka nsembe apsompsone mafano a ana ang’ombe.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena