Ekisodo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima, inu Yehova, chonde, Yehova ayende nafe pakati pathu,+ chifukwa anthuwa ndi ouma khosi,+ ndipo mutikhululukire zolakwa zathu ndi machimo athu,+ ndi kutitenga kukhala chuma chanu.”+ Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+ Salimo 106:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anapitiriza kung’ung’udza m’mahema awo,+Moti sanamvere mawu a Yehova.+
9 Kenako iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima, inu Yehova, chonde, Yehova ayende nafe pakati pathu,+ chifukwa anthuwa ndi ouma khosi,+ ndipo mutikhululukire zolakwa zathu ndi machimo athu,+ ndi kutitenga kukhala chuma chanu.”+
8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+