Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+ Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+