Deuteronomo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyezatu ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo n’kukhalabe ndi moyo.+ Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
24 Pamenepo munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyezatu ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo n’kukhalabe ndi moyo.+
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+