Ekisodo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamwamba pa phirilo. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo, ndipo Mose anakweradi.+ Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+
20 Pamenepo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamwamba pa phirilo. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo, ndipo Mose anakweradi.+
12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+