Ekisodo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Upange chovala pachifuwa chachiweruzo+ chopeta mwaluso. Uchipange mwaluso mofanana ndi efodi. Uchipange ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+
15 “Upange chovala pachifuwa chachiweruzo+ chopeta mwaluso. Uchipange mwaluso mofanana ndi efodi. Uchipange ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+