Ekisodo 38:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Golide yense amene anagwiritsidwa ntchito pa ntchito yonse ya pamalo oyera, anali woperekedwa monga nsembe yoweyula.*+ Muyezo wake unali matalente 29 ndi masekeli 730 pamuyezo wolingana ndi sekeli+ la kumalo oyera.*+
24 Golide yense amene anagwiritsidwa ntchito pa ntchito yonse ya pamalo oyera, anali woperekedwa monga nsembe yoweyula.*+ Muyezo wake unali matalente 29 ndi masekeli 730 pamuyezo wolingana ndi sekeli+ la kumalo oyera.*+