Ekisodo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo iwe ulankhule ndi anthu onse aluso amene ndinadzaza mzimu wa nzeru+ m’mitima yawo kuti amupangire Aroni zovala zomuyeretsa, kuti atumikire monga wansembe wanga.+ Ekisodo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo inetu ndaika Oholiabu mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani+ kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa munthu aliyense waluso, kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+ Ekisodo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Onse aluso+ pakati panu abwere ndi kupanga zinthu zonse zimene Yehova walamula.
3 Ndipo iwe ulankhule ndi anthu onse aluso amene ndinadzaza mzimu wa nzeru+ m’mitima yawo kuti amupangire Aroni zovala zomuyeretsa, kuti atumikire monga wansembe wanga.+
6 Ndipo inetu ndaika Oholiabu mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani+ kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa munthu aliyense waluso, kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+