Genesis 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Choncho Isiraeli ndi onse a m’nyumba yake ananyamuka kupita ku Beere-seba.+ Kumeneko iye anapereka nsembe kwa Mulungu wa bambo ake Isaki.+ Ekisodo 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ife tidzapita ulendo wamasiku atatu m’chipululu, ndipo kumeneko tikapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu, monga momwe watiuzira.”+
46 Choncho Isiraeli ndi onse a m’nyumba yake ananyamuka kupita ku Beere-seba.+ Kumeneko iye anapereka nsembe kwa Mulungu wa bambo ake Isaki.+
27 Ife tidzapita ulendo wamasiku atatu m’chipululu, ndipo kumeneko tikapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu, monga momwe watiuzira.”+