Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 8:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zoyera,+ ndi zina mwa zouluka zonse zoyera,+ n’kuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+

  • Ekisodo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+

  • Ekisodo 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ukadzatero adzamvera mawu ako.+ Pamenepo, iweyo ndi akulu a Isiraeli mudzapite kwa mfumu ya Iguputo ndi kuiuza kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi+ walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tiyende ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.’+

  • Ekisodo 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi mliri kapena lupanga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena