Ekisodo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kumeneko ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wonena kuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire m’chipululu,”+ koma kufikira tsopano sukundimvera. Ekisodo 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ife tidzapita ulendo wamasiku atatu m’chipululu, ndipo kumeneko tikapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu, monga momwe watiuzira.”+ Ekisodo 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso ziweto zathu tipita nazo.+ Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tiyenera kukatengapo zina ndi kukazigwiritsa ntchito polambira Yehova Mulungu wathu.+ Pakali pano sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”+
16 Kumeneko ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wonena kuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire m’chipululu,”+ koma kufikira tsopano sukundimvera.
27 Ife tidzapita ulendo wamasiku atatu m’chipululu, ndipo kumeneko tikapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu, monga momwe watiuzira.”+
26 Komanso ziweto zathu tipita nazo.+ Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tiyenera kukatengapo zina ndi kukazigwiritsa ntchito polambira Yehova Mulungu wathu.+ Pakali pano sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”+