Ekisodo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi mliri kapena lupanga.”+
3 Koma iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi mliri kapena lupanga.”+