Deuteronomo 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzachititsa mliri kukumamatira kufikira atakufafaniza m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+ 2 Mafumu 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo.
21 Yehova adzachititsa mliri kukumamatira kufikira atakufafaniza m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+
25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo.