-
Yeremiya 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 N’chifukwa chake mkango wa m’nkhalango wawaukira, mmbulu wa m’chipululu ukupitirizabe kuwawononga+ ndipo kambuku* akukhalabe tcheru pa mizinda yawo.+ Aliyense wotuluka m’mizindayo amakhadzulidwakhadzulidwa, chifukwa zolakwa zawo zachuluka ndipo zochita zawo za kusakhulupirika zawonjezeka kwambiri.+
-