Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+

  • Yesaya 59:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+ ndipo tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Pakuti zolakwa zathu zili pa ife, ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+

  • Ezekieli 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Oholiba anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule+ mpaka kufika pokumbukira masiku amene anali kamtsikana,+ pamene anali kuchita uhule m’dziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena