Ezekieli 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zake zonyansa zimene amaziyang’anitsitsa pozilambira+ ndipo musadziipitse ndi mafano onyansa a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+
7 Ine ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zake zonyansa zimene amaziyang’anitsitsa pozilambira+ ndipo musadziipitse ndi mafano onyansa a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+