Ezekieli 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+ Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+
25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+
4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+