Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo muzim’pereka nsembe m’mawa. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo winayo, muzim’pereka nsembe madzulo kuli kachisisira.*+

  • Deuteronomo 14:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Kumapeto kwa zaka zitatu uzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zako zonse m’chaka chimenecho,+ ndipo uzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.

  • Deuteronomo 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ukamaliza kusonkhanitsa chakhumi chonse+ cha zokolola zako m’chaka chachitatu,+ chaka chopereka chakhumi, uzikapereka chakhumicho kwa Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye. Amenewa azidzadya ndi kukhuta chakhumicho m’mizinda yanu.+

  • Hoseya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwo anali kupereka nsembe zanyama ngati mphatso kwa ine+ ndipo anali kuzidya, koma ine Yehova sindinakondwere nazo.+ Tsopano ndidzakumbukira zolakwa zawo. Ndidzawaimba mlandu chifukwa cha machimo awo+ ndiponso chifukwa chakuti iwo anabwerera ku Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena