Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+

  • Hoseya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kwambiri kumeneko.+ Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Sindidzapitiriza kuwakonda.+ Akalonga awo onse akuchita makani.+

  • Amosi 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena