Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+

  • Ezekieli 20:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “Inu a nyumba ya Isiraeli, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pitani, aliyense wa inu akatumikire mafano ake onyansawo.+ Pambuyo pake, ngati simundimvera ndidzakusiyani ndipo simudzadetsanso dzina langa loyera ndi mphatso zanu ndiponso mafano anu onyansa.’+

  • Hoseya 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwo amapereka nsembe pamwamba pa mapiri+ ndipo amafukiza nsembe zautsi pazitunda.+ Amachitanso zimenezi pansi pa zimitengo zikuluzikulu, mitengo ya mlanje, ndi mitengo yaikulu, chifukwa ili ndi mthunzi wabwino.+ N’chifukwa chake ana anu aakazi amachita dama ndipo apongozi anu aakazi amachita chigololo.

  • Amosi 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena