Oweruza 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.” Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+ Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+
14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.”
4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+