Salimo 104:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munapanga mdima kuti kukhale usiku.+Nyama zonse zakutchire zimayendayenda usikuwo. Zefaniya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+
3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+