Genesis 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mulungu anatcha kuwalako Usana,+ koma mdimawo anautcha Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku loyamba. Salimo 74:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu.+Inu munapanga chounikira, munapanga dzuwa.+ Yesaya 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+ Ndimabweretsa mtendere+ ndiponso tsoka.+ Ine Yehova ndimapanga zonsezi.+
5 Ndiyeno Mulungu anatcha kuwalako Usana,+ koma mdimawo anautcha Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku loyamba.
7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+ Ndimabweretsa mtendere+ ndiponso tsoka.+ Ine Yehova ndimapanga zonsezi.+