Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pake, munthu wina amene anathawa anafika kwa Abulamu Mheberi.+ Pa nthawiyo n’kuti Abulamu akukhala m’hema wake pakati pa mitengo ikuluikulu. Mitengoyo mwiniwake anali Mamure, yemwe anali Muamori.+ Ameneyu anali m’bale wake wa Esikolo, ndipo analinso m’bale wake wa Aneri.+ Iwowa anapanga ubale ndi Abulamu.

  • Genesis 40:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuti ndipezeke kuno anachita chondiba kudziko la Aheberi,+ ndiponso kuno palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire m’ndende muno.”+

  • Ekisodo 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Udzakana kundigonjera kufikira liti?+ Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena