Levitiko 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ngati akupereka nkhosa+ kapena mbuzi kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka+ mwana wamphongo wopanda chilema.+ Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+ Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo. Deuteronomo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muzigwiritsa ntchito miyala yathunthu pomangira Yehova Mulungu wanu guwa lansembe, ndipo muzipereka nsembe zopsereza kwa Yehova Mulungu wanu paguwalo.+
10 “‘Ngati akupereka nkhosa+ kapena mbuzi kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka+ mwana wamphongo wopanda chilema.+
14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+
11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.
6 Muzigwiritsa ntchito miyala yathunthu pomangira Yehova Mulungu wanu guwa lansembe, ndipo muzipereka nsembe zopsereza kwa Yehova Mulungu wanu paguwalo.+