Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+ Ekisodo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+
19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+