Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Adzakupatsani mneneri poyankha zonse zimene munapempha Yehova Mulungu wanu ku Horebe, tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Munapempha kuti, ‘Tiloleni tisamvenso mawu a Yehova Mulungu wathu, ndipo tisaonenso moto waukulu uwu, kuopera kuti tingafe.’+

  • Machitidwe 7:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.

  • Agalatiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nanga tsopano Chilamulo chinakhalapo chifukwa chiyani? Anachiwonjezerapo kuti machimo aonekere,+ mpaka amene ali mbewuyo atafika,+ amene anapatsidwa lonjezolo. Ndipo Chilamulocho chinaperekedwa kudzera mwa angelo,+ kudzeranso m’dzanja la mkhalapakati.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena