Genesis 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nyama zilizonse zosadetsedwa utengepo zokwanira 7, yamphongo ndi yaikazi yake.+ Koma pa nyama zilizonse zodetsedwa utengepo ziwiri zokha, yamphongo ndi yaikazi yake. Levitiko 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse+ ndi nyama, mbalame kapena chilichonse choyenda padziko lapansi, chimene ine ndachipatula kuti musadye pogamula kuti ndi chodetsedwa. Deuteronomo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya nyama zimene muyenera kudya ndi izi:+ ng’ombe, nkhosa, mbuzi,
2 Pa nyama zilizonse zosadetsedwa utengepo zokwanira 7, yamphongo ndi yaikazi yake.+ Koma pa nyama zilizonse zodetsedwa utengepo ziwiri zokha, yamphongo ndi yaikazi yake.
25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse+ ndi nyama, mbalame kapena chilichonse choyenda padziko lapansi, chimene ine ndachipatula kuti musadye pogamula kuti ndi chodetsedwa.