Levitiko 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Mose anaitana Aroni ndi ana ake ndi kuwalamula kuti asambe.+ Aefeso 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndipo anauyeretsa+ pousambitsa m’madzi a mawu a Mulungu.+ Aheberi 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka+ kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ kosatha.
28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka+ kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ kosatha.