Nahumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tunga madzi kuti upange chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ Limbitsa malo ako okhala ndi mpanda wolimba kwambiri.+ Lowa m’matope ndi kupondaponda dothi. Gwira chikombole.
14 Tunga madzi kuti upange chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ Limbitsa malo ako okhala ndi mpanda wolimba kwambiri.+ Lowa m’matope ndi kupondaponda dothi. Gwira chikombole.