2 Mbiri 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 anagwirizana ndi akalonga ake+ ndi amuna ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo,+ choncho iwo anamuthandiza. 2 Mbiri 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero anthu ambiri anasonkhana ndipo anapita kukatseka akasupe onse ndi mtsinje+ umene unkasefukira kudutsa pakati pa dzikolo, popeza anati: “Sitikufuna kuti mafumu a Asuri akabwera adzapeze madzi ochuluka.”
3 anagwirizana ndi akalonga ake+ ndi amuna ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo,+ choncho iwo anamuthandiza.
4 Chotero anthu ambiri anasonkhana ndipo anapita kukatseka akasupe onse ndi mtsinje+ umene unkasefukira kudutsa pakati pa dzikolo, popeza anati: “Sitikufuna kuti mafumu a Asuri akabwera adzapeze madzi ochuluka.”