Yoswa 21:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ana a Merari,+ omwe anatsala pa mabanja a Alevi, anapatsidwa mizinda yokwana 12 potsata mabanja awo, mwa kuchita maere. 1 Mbiri 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Merari anali Mali ndi Musi.+ Mabanja a Alevi potsatira mayina a makolo awo ndi awa:+
40 Ana a Merari,+ omwe anatsala pa mabanja a Alevi, anapatsidwa mizinda yokwana 12 potsata mabanja awo, mwa kuchita maere.