Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Levitiko 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamupondereze ndi kumuchitira nkhanza,+ ndipo muziopa Mulungu wanu.+ Levitiko 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo.+ Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.+ Miyambo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+ Yesaya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 amene anali kumenya mwaukali anthu a mitundu yosiyanasiyana powakwapula mosalekeza,+ ndiponso amene anali kugonjetsa mitundu ya anthu mokwiya, ndi chizunzo chopanda malire.+
13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo.+ Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.+
2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+
6 amene anali kumenya mwaukali anthu a mitundu yosiyanasiyana powakwapula mosalekeza,+ ndiponso amene anali kugonjetsa mitundu ya anthu mokwiya, ndi chizunzo chopanda malire.+