Salimo 107:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma akuteteza munthu wosauka ku nsautso,+Ndipo akumuchulukitsa kukhala mabanja ambiri ngati gulu la nkhosa.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+
41 Koma akuteteza munthu wosauka ku nsautso,+Ndipo akumuchulukitsa kukhala mabanja ambiri ngati gulu la nkhosa.+