Ekisodo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzombelo lidzakuta nthaka yonse ndipo simudzatha kuona dothi. Lidzadya chilichonse chotsalira. Ndithu, lidzadya chilichonse chimene matalala anakusiyirani. Ndipo lidzadya mitengo yanu yonse imene yaphuka.+
5 Dzombelo lidzakuta nthaka yonse ndipo simudzatha kuona dothi. Lidzadya chilichonse chotsalira. Ndithu, lidzadya chilichonse chimene matalala anakusiyirani. Ndipo lidzadya mitengo yanu yonse imene yaphuka.+