-
1 Mafumu 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tsopano mfumuyo inauza munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Chonde! Khazikani pansi mtima wa Yehova Mulungu wanu. Mundipempherere kuti dzanja langa libwerere mwakale.”+ Choncho munthu wa Mulungu woona uja anakhazikadi pansi+ mtima wa Yehova, moti dzanja la mfumu linabwerera mwakale, n’kukhala ngati mmene linalili poyamba.+
-