Genesis 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tikatero, katundu wawo, chuma chawo ndi ziweto zawo zonse sizidzakhala zathu kodi?+ Tiyeni tilolere zimene akufunazo kuti azikhala nafe.”+ Ekisodo 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Farao anawayankha kuti: “Ngati ndingalole n’komwe kuti inu pamodzi ndi ana anu mupite,+ ndiye kuti Yehova alidi ndi inu. Ndikudziwatu kuti zolinga zanu ndi zoipa.+
23 Tikatero, katundu wawo, chuma chawo ndi ziweto zawo zonse sizidzakhala zathu kodi?+ Tiyeni tilolere zimene akufunazo kuti azikhala nafe.”+
10 Farao anawayankha kuti: “Ngati ndingalole n’komwe kuti inu pamodzi ndi ana anu mupite,+ ndiye kuti Yehova alidi ndi inu. Ndikudziwatu kuti zolinga zanu ndi zoipa.+