Ekisodo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+ Salimo 135:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+
12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+
8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+