Ekisodo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako oyang’anira ntchito+ a Farao anamenya+ akapitawo a ana a Isiraeli amene iwo anawaika, n’kumati: “N’chifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa+ zimene munauzidwa ngati mmene munali kuchitira kale?”+
14 Kenako oyang’anira ntchito+ a Farao anamenya+ akapitawo a ana a Isiraeli amene iwo anawaika, n’kumati: “N’chifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa+ zimene munauzidwa ngati mmene munali kuchitira kale?”+