Ekisodo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano m’masiku amenewo pamene Mose anali kukula ndi kukhala wamphamvu, anapita kwa abale ake kuti akaone ntchito imene anali kugwira.+ Kumeneko anaona m’bale wake wachiheberi akumenyedwa ndi Mwiguputo.+ Machitidwe 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ataona winawake akuzunzidwa, anamutchinjiriza ndi kupha Mwiguputo wozunzayo pobwezera m’malo mwa wozunzidwa uja.+
11 Tsopano m’masiku amenewo pamene Mose anali kukula ndi kukhala wamphamvu, anapita kwa abale ake kuti akaone ntchito imene anali kugwira.+ Kumeneko anaona m’bale wake wachiheberi akumenyedwa ndi Mwiguputo.+
24 Ataona winawake akuzunzidwa, anamutchinjiriza ndi kupha Mwiguputo wozunzayo pobwezera m’malo mwa wozunzidwa uja.+