Ekisodo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anayang’ana uku ndi uku ndipo anaona kuti palibe amene akumuona. Choncho anapha Mwiguputoyo ndi kum’bisa mumchenga.+
12 Pamenepo anayang’ana uku ndi uku ndipo anaona kuti palibe amene akumuona. Choncho anapha Mwiguputoyo ndi kum’bisa mumchenga.+