Machitidwe 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ataona winawake akuzunzidwa, anamutchinjiriza ndi kupha Mwiguputo wozunzayo pobwezera m’malo mwa wozunzidwa uja.+ Aheberi 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwa chikhulupiriro, Mose atakula+ anakana kutchedwa mwana wa mwana wamkazi wa Farao,+
24 Ataona winawake akuzunzidwa, anamutchinjiriza ndi kupha Mwiguputo wozunzayo pobwezera m’malo mwa wozunzidwa uja.+