Ekisodo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana uja anakula. Kenako anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anam’patsa dzina lakuti Mose* n’kunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula m’madzi.”+ Machitidwe 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma pamene anamusiya yekha, mwana wamkazi wa Farao anamutola ndi kumulera ngati mwana wake.+
10 Mwana uja anakula. Kenako anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anam’patsa dzina lakuti Mose* n’kunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula m’madzi.”+