Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma azitenga mbalame inayo pamodzi ndi nthambi ya mtengo wa mkungudza, ulusi wofiira kwambiri ndi kamtengo ka hisope, n’kuziviika pamodzi ndi mbalame yamoyo ija m’magazi a mbalame imene aiphera pamwamba pa madzi otunga kumtsinje ija.

  • Salimo 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndiyeretseni ndi hisope ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+

      Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa chipale chofewa.+

  • Aheberi 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti pamene Mose anatchulira anthu onsewo lamulo lililonse malinga ndi Chilamulo,+ anatenga magazi a ng’ombe zazing’ono zamphongo ndi magazi a mbuzi, pamodzi ndi madzi, ubweya wa nkhosa wofiira kwambiri, ndi timitengo ta hisope,+ n’kuwaza bukulo ndi anthu onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena