Genesis 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Abulamu anauza Loti+ kuti: “Chonde, pasakhale mkangano uliwonse pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa abusa anga ndi abusa ako, pajatu ndife pachibale.+ Machitidwe 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+
8 Chotero Abulamu anauza Loti+ kuti: “Chonde, pasakhale mkangano uliwonse pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa abusa anga ndi abusa ako, pajatu ndife pachibale.+
26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+