Genesis 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+ Machitidwe 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+ Agalatiya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso ineyo ndikuti: Chilamulo chimene chinadzakhalapo zaka 430+ pambuyo pa panganolo, limene kalekalelo linatsimikizidwa ndi Mulungu,+ sichingathetse mphamvu ya panganolo, kapena kufafaniza lonjezolo.+
13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+
6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+
17 Komanso ineyo ndikuti: Chilamulo chimene chinadzakhalapo zaka 430+ pambuyo pa panganolo, limene kalekalelo linatsimikizidwa ndi Mulungu,+ sichingathetse mphamvu ya panganolo, kapena kufafaniza lonjezolo.+