Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pasatsaleko iliyonse yoti ifike m’mawa,+ ndipo asaphwanye fupa lake lililonse.+ Aikonze motsatira malamulo onse a pasika.+

  • Salimo 34:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Amateteza mafupa onse a wolungamayo.

      Ndipo palibe fupa ngakhale limodzi limene lathyoledwa.+

  • Yohane 19:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma atafika pa Yesu, sanamuthyole miyendo poona kuti wafa kale.

  • Yohane 19:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kwenikweni izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, pamene linati: “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena