Ekisodo 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Muzidyera m’nyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse. Komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+ Salimo 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amateteza mafupa onse a wolungamayo.Ndipo palibe fupa ngakhale limodzi limene lathyoledwa.+ Yohane 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwenikweni izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, pamene linati: “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.”+
46 Muzidyera m’nyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse. Komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+
36 Kwenikweni izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, pamene linati: “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.”+