Ekisodo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake panali chinthu chooneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, choyera ngati kumwamba.+ Levitiko 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mose anati: “Mverani zimene Yehova walamula kuti muchite, kuti ulemerero wa Yehova uonekere kwa inu.”+ Numeri 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+ Yohane 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yesu anati: “Kodi sindinakuuze kuti ngati ukhulupirira udzaona ulemerero wa Mulungu?”+
10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake panali chinthu chooneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, choyera ngati kumwamba.+
6 Ndiyeno Mose anati: “Mverani zimene Yehova walamula kuti muchite, kuti ulemerero wa Yehova uonekere kwa inu.”+
42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+